Psalms 20:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano ndikudziŵa kuti Chauta adzathandiza wodzozedwa wake. Adzamuyankha ali ku malo ake oyera kumwamba, pakumpambanitsa kwathunthu ndi dzanja lake lamanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano ndidziwa kuti Yehova apulumutsa wodzozedwa wake; adzamvomereza m'Mwamba mwake moyera ndi mphamvu ya chipulumutso cha dzanja lake lamanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake; Iye amamuyankha kuchokera kumwamba ku malo ake opatulika ndi mphamvu yopulumutsa ya dzanja lake lamanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsopano ndidziwa kuti Yehova apulumutsa wodzozedwa wace; Adzambvomereza m'Mwamba mwace moyera Ndi mphamvu ya cipulumutso ca dzanja lace lamanja.