Psalms 21:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumuyo idzaononga ana ao pa dziko lapansi, zidzukulu zao zidzatha pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzaziononga zobala zao kuzichotsa pa dziko lapansi, ndi mbeu zao mwa ana a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mudzawononga ana awo pa dziko lapansi, zidzukulu zawo pakati pa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzaziononga zobala zao kuzicotsa pa dziko lapansi, Ndi mbeu zao mwa ana a anthu.