Psalms 21:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akafuna kuti aichite choipa ndi kuipweteka, adzalephereratu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale iwo akukonzereni chiwembu mwa kuchenjera kwawo sadzapambana;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anakupangirani coipa: Anapangana ciwembu, osakhoza kucicita.