Psalms 21:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyo idakupemphani moyo, ndipo Inu mudaipatsa moyo wautali, wamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakupemphani moyo, mwampatsa iye; mwamtalikitsira masiku kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakupemphani moyo, ndipo munamupatsa masiku ochuluka kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakupemphani moyo, mwampatsa iye; Mwamtalikitsira masiku ku nthawi za nthawi.