Psalms 21:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, mwaisandutsa yodala kopambana mpaka muyaya. Mwaisangalatsa ndi chimwemwe, chifukwa muli nayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi Inu mwayipatsa madalitso amuyaya, Inu mwayipatsa chisangalalo ndi chimwemwe chimene chili pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mumuikira madalitso ku nthawi zonse; Mumkondweretsa ndi cimwemwe pankhope panu.