Psalms 21:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ikangotulukira, idzaŵaononga monga m'mene ng'anjo yamoto imaonongera. Chauta adzaŵatha phu, chifukwa cha kukwiya nawo, ndipo iwo adzanyeka ndi moto kuchita kuti psiti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzawaika ngati ng'anjo yamoto pa nyengo ya mkwiyo wanu. Yehova adzawatha m'kukwiya kwake, ndipo moto udzawanyeketsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi ya kuonekera kwanu mudzawasandutsa ngʼanjo yamoto yotentha. Mu ukali wake Yehova adzawameza, ndipo moto wake udzawatha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzawaika ngati ng'anjo yamoto pa nyengo ya mkwiyo wanu. Yehova adzawatha m'kukwiya kwace, Ndipo moto udzawanyeketsa.