Psalms 22:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakhala ndikudalira Inu chibadwire changa, Inu mwakhala Mulungu wanga kuyambira pamene mai wanga adandibala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chibadwire ine anandisiyira Inu, kuyambira kwa mai wanga Mulungu wanga ndinu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chibadwire ine ndinaperekedwa kwa Inu; kuchokera mʼmimba mwa amayi anga Inu mwakhala muli Mulungu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cibadwire ine anandisiyira Inu: Kuyambira kwa mai wanga Mulungu wanga ndinu.