Psalms 22:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Andiyasamira kukamwa, ngati mkango wobangula wofuna kundikadzula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Andiyasamira m'kamwa mwao, ngati mkango wozomola ndi wobangula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikango yobangula pokadzula nyama, yatsekula kwambiri pakamwa pawo kulimbana nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Andiyasamira m'kamwa mwao, Ngati mkango wozomola ndi wobangula.