Psalms 22:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moyo wanga watayika ngati madzi, mafupa anga aweyeseka. Mtima wanga uli ngati sera, wasungunuka m'kati mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndathiridwa pansi monga madzi, ndipo mafupa anga onse anaguluka. Mtima wanga ukunga sera; wasungunuka m'kati mwa matumbo anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndatayika pansi ngati madzi ndipo mafupa anga onse achoka mʼmalo mwake. Mtima wanga wasanduka phula; wasungunuka mʼkati mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndathiridwa pansi monga madzi, Ndipo mafupa anga onse anaguluka: Mtima wanga ukunga sera; Wasungunuka m'kati mwa matumbo anga,