Psalms 22:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ankhanza andizinga ngati mimbulu. Aboola manja anga ndi mapazi anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti andizinga agalu, msonkhano wa oipa wanditsekereza; andiboola m'manja anga ndi m'mapazi anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Agalu andizungulira; gulu la anthu oyipa landizinga. Alasa manja ndi mapazi anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti andizinga agaru: Msonkhano wa oipa wanditsekereza; Andiboola m'manja anga ndi m'mapazi anga.