Psalms 22:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafupa anga akuwonekera, koma anthu aja akungondiyang'anitsitsa akukondwera poona kuti ndikuvutika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikhoza kuwerenga mafupa anga onse; iwo ayang'ana nandipenyetsetsa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine nditha kuwerenga mafupa anga onse; anthu amandiyangʼanitsitsa ndi kundidzuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikhoza kuwerenga mafupa anga onse; Iwo ayang'ana nandipenyetsetsa ine: