Psalms 22:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu Chauta musakhale kutali. Inu, mphamvu zanga, fulumirani kudzandithandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, musakhale kutali; Inu mphamvu yanga, bwerani msanga kuti mudzandithandize.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu, Yehova, musakhale kutari; Mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza.