Psalms 22:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wanga, ine ndimalira usana, koma Inu simundiyankha, ndimalira usiku, koma sindipeza mpumulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simuvomereza; ndipo usiku, sindikhala chete.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Mulungu wanga, ine ndimalira masana, koma simuyankha, usikunso, ndipo sindikhala chete.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simubvomereza; Ndipo usiku, sindikhala cete.