Psalms 22:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pulumutsani moyo wanga ku lupanga. Landitseni ku mphamvu za mimbulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Landitsani moyo wanga kulupanga; wokondedwa wanga kumphamvu ya galu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pulumutsani moyo wanga ku lupanga, moyo wanga wopambanawu ku mphamvu ya agalu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Landitsani moyo wanga kulupanga; Wokondedwa wanga ku mphamvu ya garu,