Psalms 22:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pulumutseni kukamwa kwa mkango, mulanditse moyo wanga wovutika ku nyanga za njati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipulumutseni m'kamwa mwa mkango; inde mwandiyankha ine ndili pa nyanga za njati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndilanditseni mʼkamwa mwa mikango; pulumutseni ku nyanga za njati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipulumutseni m'kamwa mwa mkango; Inde mwandiyankha ine ndiri pa nyanga za njati,