Psalms 22:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ozunzika adzadya ndi kukhuta, ofunafuna Chauta adzamtamanda. Ine ndidzati, “Mitima yanu ikhale ndi moyo nthaŵi zonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ozunzika adzadya nadzakhuta, adzayamika Yehova iwo amene amfuna, ukhale moyo mtima wako nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Osauka adzadya ndipo adzakhuta; iwo amene amafunafuna Yehova adzamutamanda. Mitima yanu ikhale ndi moyo mpaka muyaya!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ozunzika adzadya nadzakhuta: Adzayamika Yehova iwo amene amfuna: Ukhale moyo mtima wako nthawi zonse.