Psalms 22:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mitundu yonse pa dziko lapansi adzakumbukira nadzatembenukira kwa Chauta, mabanja a mitundu ina ya anthu adzampembedza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Malekezero onse a dziko lapansi adzakumbukira nadzatembenukira kwa Yehova, ndipo mafuko onse a amitundu adzagwadira pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malekezero onse a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kutembenukira kwa Iye, ndipo mabanja a mitundu ya anthu adzawerama pamaso pake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Malekezero onse a dziko lapansi adzakumbukila nadzatembenukira kwa Yehova: Ndipo mafuko onse a amitundu adzagwadira pamaso panu.