Psalms 22:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ulamuliro ndi wake wa Chauta, Iye amalamula anthu a mitundu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ufumuwo ngwa Yehova; Iye achita ufumu mwa amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti ulamuliro ndi wake wa Yehova ndipo Iye amalamulira anthu a mitundu yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ufumuwo ngwa Yehova; Iye acita ufumu mwa amitundu.