Psalms 22:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzalalika za chipulumutso chake kwa anthu amene mpaka tsopano sanabadwe, ponena kuti Chauta ndiye adapulumutsa anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo adzadza nadzafotokozera chilungamo chake kwa anthu akadzabadwa, kuti Iye anachichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzalengeza za chilungamo chake kwa anthu amene pano sanabadwe pakuti Iye wachita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo adzadza nadzafotokozera cilungamo cace Kwa anthu akadzabadwa, kuti Iye anacicita.