Psalms 22:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo athu ankadalira Inu. Zoonadi, ankakhulupirira Inu, ndipo Inu munkaŵapulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Makolo athu anakhulupirira Inu; anakhulupirira, ndipo munawalanditsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa inu makolo athu anadalira; iwo anadalira ndipo Inu munawapulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Makolo athu anakhulupirira Inu: Anakhulupirira, ndipo munawalanditsa.