Psalms 22:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndine nyongolotsi, sindine munthu konse, ndine amene anthu onse amandinyodola ndi kundinyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndine nyongolotsi, si munthu ai, chotonza cha anthu, ndi wonyozedwa ndi anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine ndine nyongolotsi osati munthu, wosekedwa ndi wonyozedwa ndi anthu onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndine nyongolotsi, si munthu ai: Cotonza ca anthu, ndi wonyozedwa ndi anthu.