Psalms 22:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse ondiwona amandiseka, amandikwenzulira ndi kupukusa mitu yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onse akundipenya andiseka; akwenzula, apukusa mutu, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse amene amandiona amandiseka; amandiyankhulira mawu achipongwe akupukusa mitu yawo kunena kuti
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onse akundipenya andiseka: Akwenzula, apukusa mutu, nati,