Psalms 23:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumandikonzera chakudya, adani anga akuwona. Mumandilandira bwino podzoza mutu wanga ndi mafuta, mumadzaza chikho changa mpaka kusefukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga; mwandidzoza mutu wanga mafuta; chikho changa chisefuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumandikonzera chakudya adani anga akuona. Mumadzoza mutu wanga ndi mafuta; chikho changa chimasefukira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga: Mwandidzoza mutu wanga mafuta; cikho canga cisefuka.