Psalms 23:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, zokoma zanu ndi chikondi chanu zidzakhala ndi ine masiku onse a moyo wanga. Ndidzakhala m'Nyumba mwanu moyo wanga wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde ukoma ndi chifundo zidzanditsata masiku onse a moyo wanga, ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi, zokoma ndi chikondi chosasinthika zidzanditsata masiku onse a moyo wanga, ndipo ndidzakhala mʼNyumba ya Yehova kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde ukoma ndi cifundo zidzanditsata masiku onse a moyo wanga: Ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse.