Psalms 24:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lapansi ndi zonse zam'menemo ndi za Chauta, dziko lonse lapansi pamodzi ndi anthu onse okhalamo ndi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zake zomwe, dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Dziko lapansi ndi la Yehova ndi zonse zimene zili mʼmenemo, dziko ndi onse amene amakhala mʼmenemo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zace zomwe, Dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.