Psalms 24:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti iye ndi amene adaika dziko lapansi pa nyanja yaikulu, adalikhazika pa mitsinje yozama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Iye analimanga pazinyanja, nalikhazika pamadzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti Iye ndiye anayika maziko ake pa nyanja ndi kulikhazika pamwamba pa madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Iye analimanga pazinyanja, Nalikhazika pamadzi.