Psalms 24:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzalandira madalitso kwa Chauta, ndipo Mulungu Mpulumutsi wake adzagamula kuti alibe mlandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye adzalandira dalitso kwa Yehova, ndi chilungamo kwa Mulungu wa chipulumutso chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo adzalandira madalitso kwa Yehova ndipo Mulungu mpulumutsi wake adzagamula kuti alibe mlandu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye adzalandira dalitso kwa Yehova, Ndi cilungamo kwa Mulungu wa cipulumutso cace.