Psalms 25:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikupereka mtima wanga kwa Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Kwa Inu Yehova, ndipereka moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova.