Psalms 25:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu ameneyo adzakhaladi pabwino, ana ake adzalandira dziko kuti likhale choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wake udzakhala mokoma; ndi mbumba zake zidzalandira dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzakhala pa ulemerero masiku ake onse, ndipo zidzukulu zake zidzalandira dziko ngati cholowa chawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wace udzakhala mokoma; Ndi mbumba zace zidzalandira dziko lapansi.