Psalms 25:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amapalana chibwenzi ndi anthu omvera Iye, ndipo amaŵadziŵitsa chipangano chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinsinsi cha Yehova chili kwa iwo akumuopa Iye; ndipo adzawadziwitsa pangano lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amawulula chinsinsi chake kwa iwo amene amamuopa; amawulula pangano lake kwa iwowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinsinsi ca Yehova ciri kwa iwo akumuopa Iye; Ndipo adzawadziwitsa pangano lace.