Psalms 25:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundichotsere nkhaŵa za mumtima mwanga, ndipo munditulutse m'masautso anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masautso a mtima wanga akula, munditulutse m'zondipsinja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masautso a mu mtima mwanga achulukirachulukira; masuleni ku zowawa zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masautso a mtima wanga akula: Munditurutse m'zondipsinja.