Psalms 25:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani m'mene adani anga ankhalwe achulukira ndi m'mene chidani chao ndi ine chakulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penyani adani anga, popeza achuluka; ndipo andida ndi udani wachiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onani mmene adani anga achulukira ndi momwe chidani chawo ndi ine chakulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penyani adani anga, popeza acuruka; Ndipo andida ndi udani waciwawa.