Psalms 25:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tchinjirizani moyo wanga ndi kundipulumutsa. Musalole kuti andichititse manyazi, pakuti ndikuthaŵira kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sungani moyo wanga, ndilanditseni, ndisakhale nao manyazi, pakuti ndakhulupirira Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa; musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndimathawira kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sungani moyo wanga, ndilanditseni, Ndisakhale nao manyazi, pakuti ndakhulupirira Inu.