Psalms 25:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kukhulupirika kwanga ndi kulungama kwanga kunditeteze, popeza kuti ndakukhulupirirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ungwiro ndi kuongoka mtima zindisunge, pakuti ndayembekezera Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kukhulupirika ndi kulungama kwanga kunditeteze, chifukwa chiyembekezo changa chili mwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ungwiro ndi kuongoka mtima zindisunge, Pakuti ndayembekezera Inu.