Psalms 25:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, onse okhulupirira Inu asaŵachititse manyazi, koma muchititse manyazi onse ochita dala zosakhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde, onse akuyembekezera Inu sadzachita manyazi; adzachita manyazi iwo amene achita monyenga kopanda chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene amayembekezera kwa Ambuye sadzachititsidwa manyazi koma achinyengo ndiwo adzachititsidwe manyazi ndipo sadzakhala ndi chodzitetezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde, onse akuyembekezera Inu sadzacita manyazi Adzacita manyazi iwo amene acita monyenga kopanda cifukwa.