Psalms 25:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, kumbukirani chifundo chanu ndi chikondi chanu chosasinthika, chifukwa mudaziwonetsa kuyambira kalekale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani, Yehova, nsoni zanu ndi chifundo chanu; pakuti izi nza kale lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani Inu Yehova chifundo ndi chikondi chanu chachikulu, pakuti ndi zakalekale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani, Yehova, nsoni zanu ndi cifundo canu; Pakuti izi nza kale lonse,