Psalms 25:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndi wabwino ndi wolungama. Nchifukwa chake amaphunzitsa ochimwa njira zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye wabwino ndi wolunjika mtima, chifukwa chake adzaphunzitsa olakwa za njira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wabwino ndi wolungama; choncho Iye akulangiza ochimwa mʼnjira yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye wabwino ndi wolunjika mtima: Cifukwa cace adzaphunzitsa olawa za njira.