Psalms 26:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimadana ndi anthu ochita zoipa, sindikhala pamodzi ndi anthu oipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidana nao msonkhano wa ochimwa, ndipo sindidzakhala nao pansi ochita zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimanyansidwa ndi msonkhano wa anthu ochita zoyipa ndipo ndimakana kukhala pansi pamodzi ndi oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidana nao msonkhano wa ocimwa, Ndipo sindidzakhala nao pansi ocita zoipa.