Psalms 26:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimasamba m'manja kuwonetsa kuti sindidachimwe, ndimakupembedzani pa guwa lanu lansembe, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzasamba manja anga mosalakwa; kuti ndizungulire guwa la nsembe lanu, Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimasamba mʼmanja mwanga kuonetsa kusalakwa kwanga ndi kupita kukatumikira pa guwa lanu la nsembe, Inu Yehova,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzasamba manja anga mosalakwa; Kuti ndizungulire guwa la nsembe lanu, Yehova: