Psalms 26:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimaimba molimbika nyimbo yothokozera, ndimalalika ntchito zanu zonse zodabwitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndimveketse mau a chiyamiko, ndi kulalikira ntchito zanu zonse zozizwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kulengeza mofuwula za matamando anu ndi kuwuza onse za ntchito zanu zodabwitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndimveketse mau a ciyamiko, Ndi kulalikira nchito zanu zonse zozizwa.