Psalms 27:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndiye muuni wanga ndi chipulumutso changa. Ndidzaopa yani? Chauta ndiye linga la moyo wanga, nanga ndichitirenji mantha?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Yehova ndiye kuunika kwanga ndi chipulumutso changa; ndidzaopa yani? Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzachita mantha ndi yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Yehova ndiye kuwunika kwanga ndi chipulumutso changa; ndidzaopa yani? Yehova ndi linga la moyo wanga; ndidzachita mantha ndi yani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye kuunika kwanga ndi cipulumutso canga; ndidzaopa yani? Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzacita mantha ndi yani?