Psalms 27:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale bambo wanga ndi mai wanga andisiye ndekha, Inu Chauta mudzandisamala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti wandisiya atate wanga ndi amai wanga, koma Yehova anditola.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale abambo ndi amayi anga anditaya Yehova adzandisamala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti wandisiya atate wanga ndi amai wanga, Koma Yehova anditola.