Psalms 27:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundiwonetse njira zanu zachifundo, Inu Chauta, munditsogolere m'njira yosalala, chifukwa ndili ndi adani ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundiphunzitse njira yanu, Yehova, munditsogolere pa njira yachidikha, chifukwa cha adani anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phunzitseni njira yanu Inu Yehova, munditsogolere mʼnjira yowongoka chifukwa cha ondizunza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundiphunzitse njira yanu, Yehova, Munditsogolere pa njira yacidikha, Cifukwa ca adani anga,