Psalms 27:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musandipereke m'manja mwa adani angawo. Mboni zonama zandiwukira, ndipo zimandiwopseza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musandipereke ku chifuniro cha akundisautsa, chifukwa zinandiukira mboni zonama ndi iwo akupumira zachiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musandipereke ku zokhumba za adani anga, pakuti mboni zambiri zauka kutsutsana nane ndipo zikundiopseza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musandipereke ku cifuniro ca akundisautsa; Cifukwa zinandiukira mboni zonama ndi iwo akupumira zaciwawa.