Psalms 27:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikhulupirira kuti ndidzaona ubwino wake wa Chauta m'dziko la amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikadapanda kukhulupirira kuti ndikaone ubwino wa Yehova m'dziko la amoyo, ndikadatani!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikutsimikiza mtima za zimenezi; ndidzaona ubwino wa Yehova mʼdziko la anthu amoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikadapanda kukhulupirira kuti ndikaone ubwino wa Yehova M'dziko la amoyo, ndikadatanil