Psalms 27:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene adani ndi amaliwongo anga andiputa kuti andiphe, adzaphunthwa ndipo adzagwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu oyipa abwera kudzalimbana nane kudzadya mnofu wanga, pamene adani anga ndi achiwembu andithira nkhondo, iwo adzapunthwa ndi kugwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pondifika ine ocita zoipa kudzadya mnofu wanga, Inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa.