Psalms 27:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu Inu mudati, “Muzifunafuna nkhope yanga.” Inu Chauta, ndidzafunafuna nkhope yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene munati, Funani nkhope yanga; mtima wanga unati kwa Inu. Nkhope yanu, Yehova, ndidzaifuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga ukuti kwa Inu, “Funafuna nkhope yake!” Nkhope yanu Yehova ndidzayifunafuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene munati, Punani nkhope yanga; mtima wanga unati kwa Inu: Nkhope yanu, Yehova, ndidzaifuna.