Psalms 28:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imvani kupempha kwanga, pamene ndikulirira Inu kuti mundithandize, pamene ndikukupembedzani pokweza manja anga ku malo anu opatulika kopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mverani mau a kupemba kwanga, pamene ndilirira Inu, pamene ndikweza manja anga kuloza ponenera panu poyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imvani kupempha chifundo kwanga pomwe ndikuyitana kwa Inu kuti mundithandize, pomwe ndikukweza manja anga kuloza ku malo anu oyeretsetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mverani mau a kupemba kwanga, pamene ndilirira Inu, Pamene ndikweza manja anga kuloza ponenera panu poyera.