Psalms 28:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chakuti iwo sasamalako ntchito za Chauta, ngakhale zimene adalenga Iye. Chauta adzaŵagumula ngati nyumba, osaŵamanganso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sasamala ntchito za Yehova, kapena machitidwe a manja ake, adzawapasula, osawamanganso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza iwowo sakhudzidwa ndi ntchito za Yehova, ndi zimene manja ake anazichita, Iye adzawakhadzula ndipo sadzawathandizanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sasamala nchito za Yehova, Kapena macitidwe a manja ace, Adzawapasula, osawamanganso.