Psalms 28:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pulumutsani anthu anu, Inu Chauta, mudalitse amene mudaŵasankha. Mukhale mbusa wao, muŵasamale mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pulumutsani anthu anu, ndi kudalitsa cholandira chanu; muwawetenso, ndi kuwanyamula nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pulumutsani anthu anu ndipo mudalitse cholowa chanu; mukhale mʼbusa wawo ndipo muwakweze kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pulumutsani anthu anu, ndi kudalitsa colandira canu: Muwawetenso, ndi kuwanyamula nthawi zonse.